Levitiko 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yambewu+ kwa Yehova, nsembe yakeyo izikhala ufa wosalala.+ Azithira mafuta ndi kuika lubani* pa ufawo. Levitiko 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Nsembe yambewu imene mudzapereka kwa Yehova ikhale yopanda chofufumitsa,+ chifukwa simuyenera kutentha mtanda wofufumitsa wa ufa wokanda ndiponso uchi,* monga nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.
2 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yambewu+ kwa Yehova, nsembe yakeyo izikhala ufa wosalala.+ Azithira mafuta ndi kuika lubani* pa ufawo.
11 “‘Nsembe yambewu imene mudzapereka kwa Yehova ikhale yopanda chofufumitsa,+ chifukwa simuyenera kutentha mtanda wofufumitsa wa ufa wokanda ndiponso uchi,* monga nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.