Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 35:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Lamula ana a Isiraeli kuti pacholowa chawo cha malo, akapatseko Alevi mizinda+ yokhalamo. Akaperekenso kwa Aleviwo malo onse odyetserako ziweto ozungulira mizindayo.+

  • Numeri 35:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mizinda imene mukawapatseyo ikachokere kwa ana a Isiraeli.+ Fuko limene likakhale ndi mizinda yambiri mukatengeko yambiri, ndipo fuko limene likakhale ndi mizinda yochepa mukatengeko yochepa.+ Fuko lililonse likapereke ina ya mizinda yake kwa Alevi malinga ndi cholowa chawo chimene akalandire.”

  • Yoswa 21:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Analankhula nawo ku Silo+ m’dziko la Kanani, kuti: “Kudzera mwa Mose, Yehova analamula kuti tipatsidwe mizinda yoti tizikhalamo, pamodzi ndi malo odyetsera ziweto ozungulira mizindayo, oti tizidyetserako ziweto zathu.”+

  • Yeremiya 32:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndiyeno Hanameli mwana wa m’bale wa bambo anga analowa m’Bwalo la Alonda+ ndipo anandipeza mogwirizana ndi mawu a Yehova. Pamenepo iye anati: “Gula munda wanga wa ku Anatoti,+ m’dziko la Benjamini,+ pakuti iweyo ndi amene uli ndi ufulu woulandira monga cholowa ndiponso uli ndi ufulu wougula. Uugule ndithu.” Atatero ndinadziwa kuti mawu amenewa anali a Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena