Levitiko 26:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Zimenezi zinachititsa kuti ine nditsutsane nawo+ ndi kuwatengera kudziko la adani awo.+ “‘Izi zinachitika kuti mwina mitima yawo yosadulidwayo+ ingadzichepetse,+ ndi kulipira chifukwa cha zolakwa zawo. Numeri 14:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mwa kuchuluka kwa masiku amene munazonda dzikolo, masiku 40,+ mudzalangidwanso kwa zaka 40+ chifukwa cha zolakwa zanu, tsiku limodzi kuwerengera chaka chimodzi, tsiku limodzi chaka chimodzi,+ kuti mudziwe kuipa kondipandukira.+
41 Zimenezi zinachititsa kuti ine nditsutsane nawo+ ndi kuwatengera kudziko la adani awo.+ “‘Izi zinachitika kuti mwina mitima yawo yosadulidwayo+ ingadzichepetse,+ ndi kulipira chifukwa cha zolakwa zawo.
34 Mwa kuchuluka kwa masiku amene munazonda dzikolo, masiku 40,+ mudzalangidwanso kwa zaka 40+ chifukwa cha zolakwa zanu, tsiku limodzi kuwerengera chaka chimodzi, tsiku limodzi chaka chimodzi,+ kuti mudziwe kuipa kondipandukira.+