Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 34:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kenako iye anati: “Tsopano ngati mwandikomera mtima, inu Yehova, chonde, Yehova ayende nafe pakati pathu,+ chifukwa anthuwa ndi ouma khosi,+ ndipo mutikhululukire zolakwa zathu ndi machimo athu,+ ndi kutitenga kukhala chuma chanu.”+

  • Levitiko 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ng’ombeyo azichita nayo ngati mmene amachitira ndi ng’ombe ya nsembe yamachimo ija. Azichita momwemo. Ndipo wansembe aziwaphimbira machimo+ awo kuti akhululukidwe.

  • Levitiko 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno wansembe aziphimba machimo+ a munthuyo pamaso pa Yehova, ndipo azikhululukidwa chilichonse mwa zonse zimene angachite zom’palamulitsa.”

  • Levitiko 19:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndiyeno wansembe aziphimba tchimo limene munthuyo wachita. Azitero popereka kwa Yehova nkhosa yamphongo ya nsembe ya kupalamula ija. Pamenepo munthuyo azikhululukidwa tchimo lakelo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena