Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ng’ombeyo azichita nayo ngati mmene amachitira ndi ng’ombe ya nsembe yamachimo ija. Azichita momwemo. Ndipo wansembe aziwaphimbira machimo+ awo kuti akhululukidwe.

  • Levitiko 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mbalame inayo aziipereka ngati nsembe yopsereza motsatira ndondomeko ya nthawi zonse.+ Choncho wansembe aziphimba machimo+ amene munthuyo wachita, ndipo azikhululukidwa.+

  • Levitiko 5:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Azibweretsa kwa wansembe nkhosa yopanda chilema kuti ikhale nsembe ya kupalamula.+ Mtengo wa nkhosayo uzikhala wofanana ndi mtengo wake woikidwiratu. Ndiyeno wansembe aziphimba machimo+ a munthuyo chifukwa cha cholakwa chimene wachita mosadziwa, ngakhale kuti sanazindikire zotsatira zake, ndipo azikhululukidwa.+

  • 1 Yohane 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Komatu, ngati tikuyenda m’kuunika ngati mmene iye alili m’kuunika,+ ndiye kuti ndife ogwirizana,+ ndipo magazi+ a Yesu Mwana wake akutiyeretsa+ ku uchimo wonse.+

  • 1 Yohane 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iye ndi nsembe+ yophimba+ machimo athu.+ Osati athu+ okha, komanso a dziko lonse lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena