Levitiko 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Koma ngati sangakwanitse kupereka nkhosa,+ azibweretsa kwa Yehova njiwa ziwiri+ kapena ana awiri a nkhunda kuti zikhale nsembe za kupalamula chifukwa cha tchimo limene wachita. Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo+ ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza. Levitiko 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Monga nsembe yake ya kupalamula, azibweretsa kwa Yehova nkhosa yamphongo yopanda chilema.+ Azipereka kwa wansembe nkhosa ya mtengo wofanana ndi mtengo umene wagamulidwa, kuti ikhale nsembe ya kupalamula.+
7 “‘Koma ngati sangakwanitse kupereka nkhosa,+ azibweretsa kwa Yehova njiwa ziwiri+ kapena ana awiri a nkhunda kuti zikhale nsembe za kupalamula chifukwa cha tchimo limene wachita. Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo+ ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza.
6 Monga nsembe yake ya kupalamula, azibweretsa kwa Yehova nkhosa yamphongo yopanda chilema.+ Azipereka kwa wansembe nkhosa ya mtengo wofanana ndi mtengo umene wagamulidwa, kuti ikhale nsembe ya kupalamula.+