Ekisodo 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako upange ndowa zake zochotsera phulusa losakanizika ndi mafuta, mafosholo ake, mbale zake zolowa, mafoloko aakulu, ndi zopalira moto zake. Ziwiya zake zonse uzipange ndi mkuwa.+ Levitiko 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Azichotsa chitsokomero ndi nthenga zake ndi kuziponya potayira phulusa losakanizika ndi mafuta,+ chakum’mawa, pafupi ndi guwa lansembe. Levitiko 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ng’ombe yonseyo aziitenga ndi kupita nayo kunja kwa msasa.+ Azipita nayo kumalo oyera kumene amataya phulusa losakanizika ndi mafuta+ ndipo aziitentha pamoto wa nkhuni.+ Azitentha ng’ombeyo kumalo otayako phulusa losakanizika ndi mafuta.
3 Kenako upange ndowa zake zochotsera phulusa losakanizika ndi mafuta, mafosholo ake, mbale zake zolowa, mafoloko aakulu, ndi zopalira moto zake. Ziwiya zake zonse uzipange ndi mkuwa.+
16 Azichotsa chitsokomero ndi nthenga zake ndi kuziponya potayira phulusa losakanizika ndi mafuta,+ chakum’mawa, pafupi ndi guwa lansembe.
12 ng’ombe yonseyo aziitenga ndi kupita nayo kunja kwa msasa.+ Azipita nayo kumalo oyera kumene amataya phulusa losakanizika ndi mafuta+ ndipo aziitentha pamoto wa nkhuni.+ Azitentha ng’ombeyo kumalo otayako phulusa losakanizika ndi mafuta.