Ekisodo 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako upange ndowa zake zochotsera phulusa losakanizika ndi mafuta, mafosholo ake, mbale zake zolowa, mafoloko aakulu, ndi zopalira moto zake. Ziwiya zake zonse uzipange ndi mkuwa.+ Levitiko 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ng’ombe yonseyo aziitenga ndi kupita nayo kunja kwa msasa.+ Azipita nayo kumalo oyera kumene amataya phulusa losakanizika ndi mafuta+ ndipo aziitentha pamoto wa nkhuni.+ Azitentha ng’ombeyo kumalo otayako phulusa losakanizika ndi mafuta. Levitiko 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno wansembe azivala zovala zake zogwirira ntchito,+ ndi kuvala kabudula wansalu+ wobisa thupi lake. Kenako azichotsa phulusa losakanizika ndi mafuta,+ la nsembe yopsereza imene izitenthedwa pamoto wa paguwa nthawi zonse, ndipo aziika phulusalo pambali pa guwa lansembe.
3 Kenako upange ndowa zake zochotsera phulusa losakanizika ndi mafuta, mafosholo ake, mbale zake zolowa, mafoloko aakulu, ndi zopalira moto zake. Ziwiya zake zonse uzipange ndi mkuwa.+
12 ng’ombe yonseyo aziitenga ndi kupita nayo kunja kwa msasa.+ Azipita nayo kumalo oyera kumene amataya phulusa losakanizika ndi mafuta+ ndipo aziitentha pamoto wa nkhuni.+ Azitentha ng’ombeyo kumalo otayako phulusa losakanizika ndi mafuta.
10 Ndiyeno wansembe azivala zovala zake zogwirira ntchito,+ ndi kuvala kabudula wansalu+ wobisa thupi lake. Kenako azichotsa phulusa losakanizika ndi mafuta,+ la nsembe yopsereza imene izitenthedwa pamoto wa paguwa nthawi zonse, ndipo aziika phulusalo pambali pa guwa lansembe.