Ekisodo 28:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndipo uwapangire makabudula ansalu ofika m’ntchafu kuti azibisa maliseche awo.+ Ekisodo 39:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno anapanga nduwira+ ya nsalu yabwino kwambiri, mipango yokongola yokulunga kumutu+ ya nsalu zabwino kwambiri ndi makabudula a nsalu+ za ulusi wopota wabwino kwambiri.
28 Ndiyeno anapanga nduwira+ ya nsalu yabwino kwambiri, mipango yokongola yokulunga kumutu+ ya nsalu zabwino kwambiri ndi makabudula a nsalu+ za ulusi wopota wabwino kwambiri.