Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 28:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 “Kenako uwombe mkanjo wamandalasi ndi ulusi wabwino kwambiri. Upangenso nduwira ya nsalu yabwino kwambiri,+ ndiponso uwombe lamba+ wa mkanjo.

  • Levitiko 16:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 “Wansembe amene adzadzozedwa+ ndi kupatsidwa mphamvu* kuti atumikire monga wansembe,+ kulowa m’malo+ mwa bambo ake, aziphimba machimo ndipo azivala zovala za nsalu.+ Zovala zimenezo ndi zopatulika.+

  • Ezara 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano anthu amene anali kugwira ntchito yomanga nyumbayo anamaliza kumanga maziko+ a kachisi wa Yehova. Atatero, ansembe ovala zovala zaunsembe+ omwe ananyamula malipenga,+ ndiponso Alevi ana a Asafu+ omwe ananyamula zinganga,+ anaimirira kuti atamande Yehova motsatira dongosolo+ limene Davide mfumu ya Isiraeli anakhazikitsa.

  • Ezekieli 44:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “‘Iwo akafuna kulowa m’tinyumba ta zipata za bwalo lamkati, azivala zovala zansalu. Asamavale zovala zaubweya wa nkhosa pamene akutumikira m’tinyumba ta zipata za bwalo lamkati komanso mkati mwenimwenimo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena