Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 6:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Nawa anthu amene Davide+ anawapatsa udindo wotsogolera kuimba panyumba ya Yehova ataikapo Likasa.+

  • 1 Mbiri 23:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Panalinso alonda 4,000 a pachipata+ ndi anthu 4,000 oimbira Yehova zitamando+ ndi zoimbira+ zimene Davide anati, “Zimenezi ndazipanga kuti tizitamandira Mulungu.”

  • 2 Mbiri 29:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pa nthawi imeneyi, Hezekiya anaika Alevi+ panyumba ya Yehova atanyamula zinganga,+ zoimbira za zingwe,+ ndi azeze.+ Iwo anali kutsatira ndondomeko yoimbira imene anaikhazikitsa Davide,+ Gadi+ yemwe anali wamasomphenya wa mfumu, ndi mneneri Natani,+ popeza ndondomekoyo inachokera kwa Yehova kudzera mwa aneneri ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena