Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Komanso muzichita chikondwerero cha zokolola, chokondwerera zipatso za ntchito ya manja anu zoyamba kucha+ zimene munabzala m’munda.+ Muzichitanso chikondwerero cha kututa kumapeto kwa chaka, pamene mututa zipatso za manja anu, zam’munda.+

  • Ekisodo 34:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Muzichita chikondwerero cha masabata ndi tirigu woyamba kucha pa nyengo yokolola tiriguyo.+ Muzichitanso chikondwerero cha zokolola kumapeto kwa chaka.+

  • Numeri 28:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “‘Ndipo pa tsiku la zipatso zoyambirira,+ pamene muzipereka nsembe yambewu zatsopano kwa Yehova, paphwando lanu la masabata,+ muzichita msonkhano wopatulika. Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse pa tsikuli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena