Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 34:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Muzichita chikondwerero cha masabata ndi tirigu woyamba kucha pa nyengo yokolola tiriguyo.+ Muzichitanso chikondwerero cha zokolola kumapeto kwa chaka.+

  • Levitiko 23:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kuchokera pa tsiku limene sabata la 7 lakwanira, pazidutsa masiku 50,+ ndipo muzipereka nsembe yambewu zatsopano+ kwa Yehova.

  • Levitiko 23:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Muzilengeza+ pa tsiku lomweli kuti muchite msonkhano wopatulika ndipo musamagwire ntchito iliyonse yolemetsa. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale kulikonse kumene mungakhale m’mibadwo yanu yonse.

  • Deuteronomo 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno uzichitira Yehova Mulungu wako+ chikondwerero cha masabata, popereka nsembe zaufulu zimene ungathe, monga mmene Yehova Mulungu wako angakudalitsire.+

  • Machitidwe 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano pa tsiku la chikondwerero cha Pentekosite,+ onse anali atasonkhana pamalo amodzi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena