Ekisodo 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Muzisunga sabata chifukwa ndi lopatulika kwa inu.+ Amene walinyoza ayenera kuphedwa ndithu.+ Aliyense wogwira ntchito pa tsikuli ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+ Numeri 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa tsiku loyamba la chikondwererocho muzichita msonkhano wopatulika.+ Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse pa tsikuli.+
14 Muzisunga sabata chifukwa ndi lopatulika kwa inu.+ Amene walinyoza ayenera kuphedwa ndithu.+ Aliyense wogwira ntchito pa tsikuli ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+
18 Pa tsiku loyamba la chikondwererocho muzichita msonkhano wopatulika.+ Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse pa tsikuli.+