Ekisodo 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ine ndidzaonekera kwa iwe pamenepo ndi kulankhula nawe kuchokera pamwamba pa chivundikiro,+ pakati pa akerubi awiriwo amene ali pamwamba pa likasa la umboni. Kuchokera pamenepo ndidzakulamula zonse zokhudza ana a Isiraeli.+ Numeri 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’zofukizirazo mudzaikemo moto ndiponso zofukiza ndi kubwera nazo pamaso pa Yehova mawa. Munthu amene Yehova ati adzamusankhe,+ ameneyo ndiye woyera. Inenso ndatopa nanu, inu ana a Levi!”+ 2 Mafumu 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Hezekiya anayamba kupemphera+ pamaso pa Yehova, kuti: “Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli+ wokhala pa akerubi,+ inu nokha ndinu Mulungu woona wa maufumu onse+ a padziko lapansi.+ Inuyo munapanga kumwamba+ ndi dziko lapansi.+
22 Ine ndidzaonekera kwa iwe pamenepo ndi kulankhula nawe kuchokera pamwamba pa chivundikiro,+ pakati pa akerubi awiriwo amene ali pamwamba pa likasa la umboni. Kuchokera pamenepo ndidzakulamula zonse zokhudza ana a Isiraeli.+
7 M’zofukizirazo mudzaikemo moto ndiponso zofukiza ndi kubwera nazo pamaso pa Yehova mawa. Munthu amene Yehova ati adzamusankhe,+ ameneyo ndiye woyera. Inenso ndatopa nanu, inu ana a Levi!”+
15 Ndiyeno Hezekiya anayamba kupemphera+ pamaso pa Yehova, kuti: “Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli+ wokhala pa akerubi,+ inu nokha ndinu Mulungu woona wa maufumu onse+ a padziko lapansi.+ Inuyo munapanga kumwamba+ ndi dziko lapansi.+