Deuteronomo 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muyenera kuphunzira zimenezi kuti muziopa+ Yehova Mulungu wanu, n’cholinga choti masiku onse a moyo wanu muzisunga mfundo zake ndi malamulo ake amene ndikukuuzani, inuyo, ana anu ndi zidzukulu zanu,+ ndiponso kuti masiku anu atalike.+ Salimo 119:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzakonda malamulo anu.+Ndipo sindidzaiwala mawu anu.+ Ezekieli 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Yendani motsatira malamulo anga+ ndipo musunge zigamulo zanga+ ndi kuzitsatira.+ 1 Yohane 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+
2 Muyenera kuphunzira zimenezi kuti muziopa+ Yehova Mulungu wanu, n’cholinga choti masiku onse a moyo wanu muzisunga mfundo zake ndi malamulo ake amene ndikukuuzani, inuyo, ana anu ndi zidzukulu zanu,+ ndiponso kuti masiku anu atalike.+
19 Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Yendani motsatira malamulo anga+ ndipo musunge zigamulo zanga+ ndi kuzitsatira.+
3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+