Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 7:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “‘Ngati akupereka lonjezo+ monga nsembe yake kapena ngati akupereka nsembe yaufulu,+ aziidya pa tsiku limene wapereka nsembeyo, ndipo angathenso kudya imene yatsala pa tsiku lotsatira.

  • Levitiko 23:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Muzichita zimenezi kuwonjezera pa kusunga masabata a Yehova,+ kupereka mphatso zanu,+ nsembe zanu zonse za lonjezo+ ndi nsembe zanu zonse zaufulu+ zimene muyenera kupereka kwa Yehova.

  • Numeri 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 popereka nsembe yotentha ndi moto kwa Yehova,+ kuti ikhale nsembe yopsereza,+ kapena nsembe yochitira lonjezo lapadera, kapena nsembe yongopereka mwaufulu,+ kapena yopereka pa nthawi ya zikondwerero zanu,+ kuti mufukize fungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova+ la nyama ya ng’ombe kapena ya nkhosa,

  • Salimo 22:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Chifukwa cha zimene mwachita ndidzakutamandani mumpingo waukulu.+

      Ndidzakwaniritsa malonjezo anga pamaso pa anthu oopa iye.+

  • Salimo 56:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Inu Mulungu, ine ndikuyenera kukwaniritsa malonjezo anga kwa inu.+

      Ndidzapereka kwa inu nsembe zoyamikira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena