Genesis 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzachulukitsa mbewu yako ngati mchenga wa padziko lapansi, kotero kuti ngati munthu angathe kuwerenga mchengawo, ndiye kuti mbewu yako idzatha kuwerengedwa.+ Genesis 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, monganso mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.+ Komanso mbewu yako idzalanda chipata* cha adani ake.+ Ekisodo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ana a Isiraeli anaberekana ndipo anachuluka m’dzikomo. Iwo anapitiriza kuchulukana ndi kukhala amphamvu koposa, moti anadzaza m’dzikomo.+
16 Ndidzachulukitsa mbewu yako ngati mchenga wa padziko lapansi, kotero kuti ngati munthu angathe kuwerenga mchengawo, ndiye kuti mbewu yako idzatha kuwerengedwa.+
17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, monganso mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.+ Komanso mbewu yako idzalanda chipata* cha adani ake.+
7 Ana a Isiraeli anaberekana ndipo anachuluka m’dzikomo. Iwo anapitiriza kuchulukana ndi kukhala amphamvu koposa, moti anadzaza m’dzikomo.+