Genesis 49:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yuda ndi mwana wa mkango.+ Umapha nyama n’kubwerako ndithu, mwana wanga. Iye amapinda mawondo ake n’kudziwongola ngati mkango utagona pansi. Ndipo monga mkango, ndani angamudzutse?+ Numeri 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anagwada pansi. Anagona pansi ngati mkango.Ngati mkango, ndani angayese kum’dzutsa?+Odalitsa iwe n’ngodalitsika,+Ndipo otemberera iwe n’ngotembereredwa.”+ Miyambo 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mkango, umene ndi wamphamvu kwambiri panyama zonse zakutchire ndiponso umene suopa chilichonse n’kubwerera m’mbuyo,+
9 Yuda ndi mwana wa mkango.+ Umapha nyama n’kubwerako ndithu, mwana wanga. Iye amapinda mawondo ake n’kudziwongola ngati mkango utagona pansi. Ndipo monga mkango, ndani angamudzutse?+
9 Iye anagwada pansi. Anagona pansi ngati mkango.Ngati mkango, ndani angayese kum’dzutsa?+Odalitsa iwe n’ngodalitsika,+Ndipo otemberera iwe n’ngotembereredwa.”+
30 Mkango, umene ndi wamphamvu kwambiri panyama zonse zakutchire ndiponso umene suopa chilichonse n’kubwerera m’mbuyo,+