Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 8:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndiyeno Yehova anamva fungo lokhazika mtima pansi,+ moti ananena mumtima+ mwake kuti: “Sindidzatembereranso nthaka+ chifukwa cha zochita za anthu, popeza maganizo+ a anthu amakhala oipa kuyambira pa ubwana wawo.+ Ndipo sindidzawononganso chilichonse monga ndachitiramu.+

  • Ekisodo 29:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Nkhosa yonseyo uitenthe paguwa lansembe. Imeneyo ndi nsembe yopsereza+ yoperekedwa kwa Yehova, fungo lokhazika mtima pansi.+ Ndiyo nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.

  • Aefeso 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 ndipo yendanibe m’chikondi,+ monganso Khristu anakukondani+ n’kudzipereka yekha chifukwa cha inu. Iye anadzipereka yekha monga chopereka+ ndiponso monga nsembe yafungo lokoma kwa Mulungu.+

  • Afilipi 4:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Komabe, ine ndili ndi zonse zimene ndimafunikira, ndipo n’zokwanira ndi zosefukira. Sindikusowa kanthu, pakuti tsopano ndalandira kwa Epafurodito+ zinthu zochokera kwa inu. Zili ngati fungo lonunkhira bwino+ ndiponso nsembe yovomerezeka+ yosangalatsa kwa Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena