Numeri 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anthuwo atachoka pa Kibiroti-hatava, anasamukira ku Hazeroti,+ ndipo anakhala kumeneko. Numeri 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pambuyo pake, anthuwo anachoka ku Hazeroti,+ n’kukamanga msasa m’chipululu cha Parana.+ Deuteronomo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Awa ndiwo mawu amene Mose analankhula ndi Aisiraeli onse m’chipululu, m’chigawo cha Yorodano,+ m’chipululu moyang’anana ndi Sufu, pakati pa Parana,+ Tofeli, Labani, Hazeroti+ ndi Dizahabi,
1 Awa ndiwo mawu amene Mose analankhula ndi Aisiraeli onse m’chipululu, m’chigawo cha Yorodano,+ m’chipululu moyang’anana ndi Sufu, pakati pa Parana,+ Tofeli, Labani, Hazeroti+ ndi Dizahabi,