Ekisodo 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Upange beseni losambira lamkuwa ndi choikapo chake chamkuwa.+ Uliike pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe, ndipo uthiremo madzi.+ Ezekieli 36:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ine ndidzakuwazani madzi oyera ndipo mudzakhala oyera. Ndidzakuyeretsani+ pokuchotserani zonyansa zanu zonse+ ndi mafano anu onse onyansa.+
18 “Upange beseni losambira lamkuwa ndi choikapo chake chamkuwa.+ Uliike pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe, ndipo uthiremo madzi.+
25 Ine ndidzakuwazani madzi oyera ndipo mudzakhala oyera. Ndidzakuyeretsani+ pokuchotserani zonyansa zanu zonse+ ndi mafano anu onse onyansa.+