Levitiko 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Nsembe yanu iliyonse yambewu muziikoleretsa ndi mchere.+ Musapereke nsembe yanu yambewu yopanda mchere wokukumbutsani pangano+ la Mulungu. Popereka nsembe yanu iliyonse muziperekanso mchere. 2 Mbiri 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi simukudziwa kuti Yehova Mulungu wa Isiraeli anapereka ufumu kwa Davide+ kuti azilamulira Isiraeli mpaka kalekale?+ Simukudziwa kodi kuti anaupereka kwa iye ndi ana ake+ pochita naye pangano losatha?*+
13 “‘Nsembe yanu iliyonse yambewu muziikoleretsa ndi mchere.+ Musapereke nsembe yanu yambewu yopanda mchere wokukumbutsani pangano+ la Mulungu. Popereka nsembe yanu iliyonse muziperekanso mchere.
5 Kodi simukudziwa kuti Yehova Mulungu wa Isiraeli anapereka ufumu kwa Davide+ kuti azilamulira Isiraeli mpaka kalekale?+ Simukudziwa kodi kuti anaupereka kwa iye ndi ana ake+ pochita naye pangano losatha?*+