Ekisodo 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ngati sanachite kum’dikirira, ndipo Mulungu woona walola kuti mwangozi munthuyo afere m’manja mwake,+ pamenepo ndidzakukonzerani malo amene angathawireko.+ Numeri 35:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mupereke mizinda itatu tsidya lino la Yorodano,+ ndiponso mukapereke mizinda itatu tsidya linalo, m’dziko la Kanani.+ Imeneyi ikakhala mizinda yothawirako. Yoswa 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho anasankha mizinda ina kuti ikhale yopatulika. Mizinda yake inali Kedesi+ ku Galileya m’dera lamapiri la Nafitali, Sekemu+ m’dera lamapiri la Efuraimu, Kiriyati-ariba,+ kutanthauza Heburoni, m’dera lamapiri la Yuda.
13 Koma ngati sanachite kum’dikirira, ndipo Mulungu woona walola kuti mwangozi munthuyo afere m’manja mwake,+ pamenepo ndidzakukonzerani malo amene angathawireko.+
14 Mupereke mizinda itatu tsidya lino la Yorodano,+ ndiponso mukapereke mizinda itatu tsidya linalo, m’dziko la Kanani.+ Imeneyi ikakhala mizinda yothawirako.
7 Choncho anasankha mizinda ina kuti ikhale yopatulika. Mizinda yake inali Kedesi+ ku Galileya m’dera lamapiri la Nafitali, Sekemu+ m’dera lamapiri la Efuraimu, Kiriyati-ariba,+ kutanthauza Heburoni, m’dera lamapiri la Yuda.