Genesis 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zitatero, Kaini anauza Abele m’bale wake kuti: “Tiye tipite kumunda.” Ali kumeneko, Kaini anam’kantha Abele m’bale wake n’kumupha.+ Numeri 35:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo ngati chifukwa chodana naye anamukankha,+ kapena ngati anamulasa ndi chinthu atamubisalira,+ mnzakeyo n’kufa, Yakobo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti amene anati: “Usachite chigololo,”+ anatinso: “Usaphe munthu.”+ Tsopano ngati iwe sunachite chigololo koma wapha munthu, walakwira chilamulo.
8 Zitatero, Kaini anauza Abele m’bale wake kuti: “Tiye tipite kumunda.” Ali kumeneko, Kaini anam’kantha Abele m’bale wake n’kumupha.+
20 Ndipo ngati chifukwa chodana naye anamukankha,+ kapena ngati anamulasa ndi chinthu atamubisalira,+ mnzakeyo n’kufa,
11 Pakuti amene anati: “Usachite chigololo,”+ anatinso: “Usaphe munthu.”+ Tsopano ngati iwe sunachite chigololo koma wapha munthu, walakwira chilamulo.