-
Rute 4:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndiye ine ndaganiza zoti ndikuuze kuti, ‘Ugule mundawo+ pamaso pa anthu ndi pamaso pa akulu a mzinda uno.+ Ngati ukufuna kuuwombola, uwombole. Koma ngati sukufuna undiuze kuti ndidziwe, popeza palibenso wina amene angauwombole koma iweyo,+ pambuyo pako pali ine.’” Pamenepo, wowombola uja anati: “Ndiuwombola ineyo.”+
-