Deuteronomo 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Usasunthe zizindikiro za malire a mnzako,+ makolo anu ataika kale malire a cholowa chimene udzalandira, m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa kuti ulitenge kukhala lako. Miyambo 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Usasunthire kumbuyo malire akalekale, amene makolo ako anaika.+ Miyambo 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usasunthire kumbuyo malire akalekale,+ ndipo usalowe m’munda mwa ana amasiye.*+
14 “Usasunthe zizindikiro za malire a mnzako,+ makolo anu ataika kale malire a cholowa chimene udzalandira, m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa kuti ulitenge kukhala lako.