Ekisodo 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Inu munaona nokha zimene ndinachitira Aiguputo,+ kuti ndikunyamuleni pamapiko a chiwombankhanga ndi kukubweretsani kwa ine.+ Deuteronomo 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Usaiope.+ Nthawi zonse uzikumbukira zimene Yehova Mulungu wako anachitira Farao ndi Iguputo yense.+ Yoswa 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Patapita nthawi, ndinatumiza Mose ndi Aroni,+ ndipo ndinagwetsera Iguputo miliri.+ Nditatero ndinakutulutsani+ ku Iguputoko.
4 ‘Inu munaona nokha zimene ndinachitira Aiguputo,+ kuti ndikunyamuleni pamapiko a chiwombankhanga ndi kukubweretsani kwa ine.+
18 Usaiope.+ Nthawi zonse uzikumbukira zimene Yehova Mulungu wako anachitira Farao ndi Iguputo yense.+
5 Patapita nthawi, ndinatumiza Mose ndi Aroni,+ ndipo ndinagwetsera Iguputo miliri.+ Nditatero ndinakutulutsani+ ku Iguputoko.