Levitiko 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo, mudzakhala mukupuntha zimene mwakolola kufikira nyengo yokolola mphesa, ndipo mudzakhala mukukolola mphesa kufikira nyengo yofesa mbewu. Mudzadya mkate wanu ndi kukhuta,+ ndipo mudzakhala otetezeka m’dziko lanu.+ Salimo 65:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu mwatembenukira dziko lapansi kuti mulipatse zinthu zochuluka,+Mwalilemeretsa kwambiri.Mtsinje wochokera kwa Mulungu ndi wosefukira ndi madzi.+Munalinganiza zinthu, kuti mbewu zawo zibale.+Umu ndi mmene mumaperekera zinthu padziko lapansi.+
5 Pamenepo, mudzakhala mukupuntha zimene mwakolola kufikira nyengo yokolola mphesa, ndipo mudzakhala mukukolola mphesa kufikira nyengo yofesa mbewu. Mudzadya mkate wanu ndi kukhuta,+ ndipo mudzakhala otetezeka m’dziko lanu.+
9 Inu mwatembenukira dziko lapansi kuti mulipatse zinthu zochuluka,+Mwalilemeretsa kwambiri.Mtsinje wochokera kwa Mulungu ndi wosefukira ndi madzi.+Munalinganiza zinthu, kuti mbewu zawo zibale.+Umu ndi mmene mumaperekera zinthu padziko lapansi.+