Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 15:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kenako anamutengera panja, n’kumuuza kuti: “Kweza maso ako kumwamba, uwerenge nyenyezizo ngati ungathe kuziwerenga.”+ Ndipo anamuuzanso kuti: “Umu ndi mmene mbewu yako idzakhalire.”+

  • Ekisodo 32:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kumbukirani Abulahamu, Isaki ndi Isiraeli atumiki anu, amene munawalumbirira pa inu mwini,+ powauza kuti, ‘Ndidzachulukitsa mbewu yanu ngati nyenyezi zakumwamba,+ ndipo dziko lonseli limene ndalipatula ndidzalipereka kwa mbewu yanu,+ kuti likhale lawo mpaka kalekale.’”+

  • Numeri 26:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Amenewa ndiwo amuna onse amene anawerengedwa pakati pa ana a Isiraeli. Onse pamodzi analipo 601,730.+

  • Deuteronomo 10:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Makolo anu anapita ku Iguputo ndi anthu 70,+ ndipo tsopano Yehova Mulungu wanu wakuchulukitsani ngati nyenyezi zakuthambo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena