Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pakuti mngelo wanga adzakutsogolera ndi kukulowetsa m’dziko la Aamori, Ahiti, Aperezi, Akanani, Ahivi ndi Ayebusi, ndipo ndidzawafafaniza ndithu.+

  • Deuteronomo 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndipo inu mukudziwa bwino lero kuti Yehova Mulungu wanu akuwoloka patsogolo panu+ kuti akutsogolereni. Iye ndi moto wowononga.+ Adzawawononga+ ndipo iye ndi amene adzawagonjetsa inu mukuona. Pamenepo mudzawalande dziko lawo ndi kuwawononga mofulumira monga mmene Yehova wakuuzirani.+

  • Deuteronomo 19:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Yehova Mulungu wako akadzawononga mitundu+ ya m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, iwe n’kuwalandadi dzikolo ndi kukhala m’mizinda yawo ndi m’nyumba zawo,+

  • Salimo 44:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Munapitikitsa anthu a mitundu ina ndi dzanja lanu,+

      Ndipo m’malo mwawo munakhazikitsa anthu anu.+

      Munagonjetsa mitundu ya anthu ndi kuipitikitsa.+

  • Salimo 78:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 Chifukwa cha iwo anachotsa mitundu ina pang’onopang’ono m’dzikoli,+

      Ndipo anayesa dzikoli ndi kuligawa kwa iwo kukhala cholowa chawo,+

      Moti anachititsa mafuko a Isiraeli kukhala m’nyumba zawozawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena