Deuteronomo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo ndi zigamulo zolungama zofanana ndi chilamulo chonsechi chimene ndikukuikirani pamaso panu lero?+ Deuteronomo 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akakhala pampando wachifumu, ayenera kukopera buku lakelake la chilamulo ichi, kuchokera m’buku limene ansembe achilevi amasunga.+ Nehemiya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Alevi anali kufotokozera anthu chilamulocho,+ anthuwo ataimirira.+ Alevi amenewo anali Yesuwa, Bani, Serebiya,+ Yamini, Akubu, Sabetai, Hodiya, Maaseya, Kelita, Azariya, Yozabadi,+ Hanani ndi Pelaya.+
8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo ndi zigamulo zolungama zofanana ndi chilamulo chonsechi chimene ndikukuikirani pamaso panu lero?+
18 Akakhala pampando wachifumu, ayenera kukopera buku lakelake la chilamulo ichi, kuchokera m’buku limene ansembe achilevi amasunga.+
7 Pamenepo Alevi anali kufotokozera anthu chilamulocho,+ anthuwo ataimirira.+ Alevi amenewo anali Yesuwa, Bani, Serebiya,+ Yamini, Akubu, Sabetai, Hodiya, Maaseya, Kelita, Azariya, Yozabadi,+ Hanani ndi Pelaya.+