17Fuko la Manase, mwana woyamba wa Yosefe,+ linapatsidwa gawo lake.+ Makiri+ mwana woyamba wa Manase,+ bambo wake wa Giliyadi,+ anali mwamuna wamphamvu pankhondo,+ ndipo gawo lake linali Giliyadi+ ndi Basana.
70 Kuchokera ku hafu ya fuko la Manase, anapatsa mabanja a ana a Kohati amene anatsala,+ mzinda wa Aneri+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Bileamu+ ndi malo ake odyetserako ziweto.