Deuteronomo 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho muwoloke Yorodano+ ndi kukhala m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kukhala lanu.+ Iye adzakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, ndipo mudzakhaladi otetezeka.+ Deuteronomo 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Motero Yehova Mulungu wanu akakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mufafanize dzina la Amaleki pansi pa thambo.+ Musaiwale zimenezi.
10 Choncho muwoloke Yorodano+ ndi kukhala m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kukhala lanu.+ Iye adzakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, ndipo mudzakhaladi otetezeka.+
19 Motero Yehova Mulungu wanu akakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mufafanize dzina la Amaleki pansi pa thambo.+ Musaiwale zimenezi.