-
Numeri 23:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Tsopano Balaki anauza Balamu kuti: “Ngati mwalephera kuwatemberera ngakhale pang’ono pokha, ndiye musawadalitsenso m’pang’ono pomwe.”
-