Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 22:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 ‘Taonani! Anthu amene achokera ku Iguputo adzaza dziko lino kulikonse kumene munthu angayang’ane.+ Tsopano bwerani, mudzanditembererere anthuwa,+ kuti mwina ndingathe kumenyana nawo n’kuwathamangitsa.’”

  • Numeri 24:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamenepo Balaki anapsera mtima Balamu n’kuwomba m’manja.+ Kenako anauza Balamu kuti: “Ndinakuitana kuti udzatemberere+ adani anga, koma iwe wawadalitsa kwambiri katatu konseka!

  • Yoswa 24:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ine sindinafune kumvera Balamu.+ Chotero, iye anakudalitsani mobwerezabwereza,+ ndipo ine ndinakulanditsani m’manja mwake.+

  • Nehemiya 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 chifukwa iwowa sanachingamire ana a Isiraeli kuti awapatse chakudya+ ndi madzi.+ M’malomwake, analemba ganyu Balamu+ kuti awatemberere.+ Koma Mulungu wathu anasintha temberero limenelo kukhala dalitso.+

  • Salimo 109:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Alekeni anditemberere,+

      Koma inu mundipatse madalitso.+

      Iwo aimirira kuti andiukire koma inu muwachititse manyazi,+

      Ndipo ine mtumiki wanu ndisangalale.+

  • Mika 6:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Inu anthu anga, chonde kumbukirani+ zimene Balaki mfumu ya Mowabu anakonza kuti achite+ ndiponso zimene Balamu mwana wa Beori anamuyankha.+ Kumbukirani zimene zinachitika kuyambira ku Sitimu+ kukafika ku Giligala.+ Zimenezo zinachitika n’cholinga chakuti zochita za Yehova zolungama zidziwike.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena