Deuteronomo 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti ndinachita mantha chifukwa cha mkwiyo waukulu wa Yehova umene unakuyakirani, mpaka kufika pofuna kukufafanizani.+ Koma Yehova anandimveranso pa nthawi imeneyi.+ 1 Mafumu 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Yehova anamva mawu a Eliya,+ moti moyo wa mwanayo unabwerera mwa iye, ndipo anakhala wamoyo.+ Salimo 113:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye amatsika m’munsi kuti aone kumwamba ndi dziko lapansi.+ Yakobo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+
19 Pakuti ndinachita mantha chifukwa cha mkwiyo waukulu wa Yehova umene unakuyakirani, mpaka kufika pofuna kukufafanizani.+ Koma Yehova anandimveranso pa nthawi imeneyi.+
22 Kenako Yehova anamva mawu a Eliya,+ moti moyo wa mwanayo unabwerera mwa iye, ndipo anakhala wamoyo.+
6 Iye amatsika m’munsi kuti aone kumwamba ndi dziko lapansi.+ Yakobo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+
16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+