Salimo 65:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+ Miyambo 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nsembe ya anthu oipa imam’nyansa Yehova,+ koma pemphero la anthu owongoka mtima limam’sangalatsa.+ Machitidwe 9:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma Petulo anatulutsa anthu onse,+ ndiyeno anagwada pansi ndi kupemphera. Kenako anatembenukira mtembowo ndi kunena kuti: “Tabita, dzuka!” Pamenepo mayiyo anatsegula maso ake, ndipo mmene anaona Petulo, anadzuka n’kukhala tsonga.+ Aheberi 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma anadziwa kuti Mulungu ali ndi mphamvu zomuukitsa kwa akufa.+ Ndipo iye anamulandiradi kuchokera kwa akufa m’njira ya fanizo.+ Yakobo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+
40 Koma Petulo anatulutsa anthu onse,+ ndiyeno anagwada pansi ndi kupemphera. Kenako anatembenukira mtembowo ndi kunena kuti: “Tabita, dzuka!” Pamenepo mayiyo anatsegula maso ake, ndipo mmene anaona Petulo, anadzuka n’kukhala tsonga.+
19 Koma anadziwa kuti Mulungu ali ndi mphamvu zomuukitsa kwa akufa.+ Ndipo iye anamulandiradi kuchokera kwa akufa m’njira ya fanizo.+
16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+