-
1 Samueli 23:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Kenako Sauli anafika ndi asilikali ake kudzafunafuna Davide.+ Davide atauzidwa zimenezi, nthawi yomweyo analowa mkatikati mwa chipululu n’kukabisala kuthanthwe,+ ndipo anapitiriza kukhala m’chipululu cha Maoni. Sauli atamva zimenezo anayamba kuthamangitsa+ Davide m’chipululu chimenecho cha Maoni.
-