Numeri 34:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Amuna amene akakugawireni malo monga cholowa chanu, mayina awo ndi awa: Wansembe Eleazara+ ndi Yoswa mwana wa Nuni.+ Yoswa 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Limeneli ndilo dziko limene ana a Isiraeli anatenga monga cholowa chawo m’dziko la Kanani.+ Wansembe Eleazara, Yoswa mwana wa Nuni, ndi atsogoleri a mafuko a makolo a ana a Isiraeli, ndiwo anagawa dzikolo kuti likhale cholowa chawo.+
17 “Amuna amene akakugawireni malo monga cholowa chanu, mayina awo ndi awa: Wansembe Eleazara+ ndi Yoswa mwana wa Nuni.+
14 Limeneli ndilo dziko limene ana a Isiraeli anatenga monga cholowa chawo m’dziko la Kanani.+ Wansembe Eleazara, Yoswa mwana wa Nuni, ndi atsogoleri a mafuko a makolo a ana a Isiraeli, ndiwo anagawa dzikolo kuti likhale cholowa chawo.+