Numeri 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mizindayo ikakhale kothawirako munthu wopha mnzake amene akuthawa wobwezera magazi,+ kuti amene wapha mnzakeyo asaphedwe kufikira ataima pamaso pa oweruza kuti aweruzidwe.+ Numeri 35:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 oweruza aweruze pakati pa wopha mnzakeyo ndi woyenera kubwezera magaziyo, malinga ndi malamulo amenewa.+
12 Mizindayo ikakhale kothawirako munthu wopha mnzake amene akuthawa wobwezera magazi,+ kuti amene wapha mnzakeyo asaphedwe kufikira ataima pamaso pa oweruza kuti aweruzidwe.+
24 oweruza aweruze pakati pa wopha mnzakeyo ndi woyenera kubwezera magaziyo, malinga ndi malamulo amenewa.+