Numeri 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mizindayo ikakhale kothawirako munthu wopha mnzake amene akuthawa wobwezera magazi,+ kuti amene wapha mnzakeyo asaphedwe kufikira ataima pamaso pa oweruza kuti aweruzidwe.+ Yoswa 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Azithawira+ kumzinda umodzi mwa mizindayi n’kukaima pachipata+ cholowera mumzindawo. Akatero azifotokoza nkhani yake kwa akulu+ a mzindawo. Akuluwo amulandire n’kumupatsa malo mumzindamo kuti azikhala nawo limodzi.
12 Mizindayo ikakhale kothawirako munthu wopha mnzake amene akuthawa wobwezera magazi,+ kuti amene wapha mnzakeyo asaphedwe kufikira ataima pamaso pa oweruza kuti aweruzidwe.+
4 Azithawira+ kumzinda umodzi mwa mizindayi n’kukaima pachipata+ cholowera mumzindawo. Akatero azifotokoza nkhani yake kwa akulu+ a mzindawo. Akuluwo amulandire n’kumupatsa malo mumzindamo kuti azikhala nawo limodzi.