Deuteronomo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Mudziikire oweruza+ ndi atsogoleri+ m’mizinda yanu yonse imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, malinga ndi mafuko anu. Oweruza ndi atsogoleriwo aziweruza anthu ndi chiweruzo cholungama. Deuteronomo 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo bambo ndi mayi a mtsikanayo azibweretsa umboni wosonyeza kuti mtsikanayo anali namwali kwa akulu a mzinda kuchipata cha mzindawo.+ Rute 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zitatero, Boazi anapita kuchipata.+ Kumeneko iye anakhala pansi. Ali chikhalire choncho, anaona wowombola anam’tchula uja+ akudutsa. Ndiyeno Boazi anati: “Iwe Uje takhotera pano, khala pansi apa.” Motero anakhota n’kukhala pansi. Yobu 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndikapita kuchipata cha mzinda,+Ndinkakonzako malo anga okhala pabwalo la mzinda.+ Miyambo 31:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mwamuna wake*+ amadziwika pazipata,+ akakhala pansi pamodzi ndi akulu a m’dzikolo.
18 “Mudziikire oweruza+ ndi atsogoleri+ m’mizinda yanu yonse imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, malinga ndi mafuko anu. Oweruza ndi atsogoleriwo aziweruza anthu ndi chiweruzo cholungama.
15 Pamenepo bambo ndi mayi a mtsikanayo azibweretsa umboni wosonyeza kuti mtsikanayo anali namwali kwa akulu a mzinda kuchipata cha mzindawo.+
4 Zitatero, Boazi anapita kuchipata.+ Kumeneko iye anakhala pansi. Ali chikhalire choncho, anaona wowombola anam’tchula uja+ akudutsa. Ndiyeno Boazi anati: “Iwe Uje takhotera pano, khala pansi apa.” Motero anakhota n’kukhala pansi.