Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Iwo akhala ngati mahatchi amphongo achilakolako champhamvu chofuna kukwera, okhala ndi mavalo amphamvu. Aliyense amamemesa* mkazi wa mnzake.+

  • Hoseya 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Aisiraeli azama nazo zinthu zowononga+ ngati m’masiku a Gibeya.+ Mulungu adzakumbukira zolakwa zawo+ ndipo adzawalanga chifukwa cha machimo awo.

  • Hoseya 10:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Inu ana a Isiraeli, mwakhala mukuchimwa kuyambira m’masiku a Gibeya+ ndipo anthu anapitirizabe kuchita machimo kumeneko. Nkhondo ya ku Gibeya yomenyana ndi anthu osalungama sinawawononge onse.+

  • Aefeso 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Popeza iwo tsopano sakuthanso kuzindikira makhalidwe abwino,+ anadzipereka okha ku khalidwe lotayirira+ kuti achite chonyansa+ chamtundu uliwonse mwadyera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena