Yoswa 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zitatero, anthu onse a mumzindawo anaitanidwa kuti akathamangitse Aisiraeli. Anthuwo anathamangitsa Aisiraeliwo limodzi ndi Yoswa, mpaka anafika kutali ndi mzinda wawo.+ Oweruza 20:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ana a Benjamini ataona kuti amuna a Isiraeli akuthawa,+ anaganiza kuti akugonja. Koma iwo anali kuthawa chifukwa anali kudalira amuna amene anawaika kuti abisalire mzinda wa Gibeya.
16 Zitatero, anthu onse a mumzindawo anaitanidwa kuti akathamangitse Aisiraeli. Anthuwo anathamangitsa Aisiraeliwo limodzi ndi Yoswa, mpaka anafika kutali ndi mzinda wawo.+
36 Ana a Benjamini ataona kuti amuna a Isiraeli akuthawa,+ anaganiza kuti akugonja. Koma iwo anali kuthawa chifukwa anali kudalira amuna amene anawaika kuti abisalire mzinda wa Gibeya.