-
Oweruza 20:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Ana a Benjamini atatuluka kuti akakumane ndi anthuwo, anakokedwera kutali ndi mzinda.+ Ndiyeno monga mmene zinachitikira maulendo oyamba aja, ana a Benjaminiwo anayamba kukantha ena mwa anthuwo, amuna a Isiraeli 30,+ pamisewu ikuluikulu yakunja kwa mzinda, ndi kuwavulaza koti sakanatha kuchira. Wina mwa misewu imeneyi unali wopita ku Beteli+ ndipo wina unali wopita ku Gibeya.+
-