Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 8:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Zitatero, anthu onse a mumzindawo anaitanidwa kuti akathamangitse Aisiraeli. Anthuwo anathamangitsa Aisiraeliwo limodzi ndi Yoswa, mpaka anafika kutali ndi mzinda wawo.+

  • Oweruza 20:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ana a Benjamini atatuluka kuti akakumane ndi anthuwo, anakokedwera kutali ndi mzinda.+ Ndiyeno monga mmene zinachitikira maulendo oyamba aja, ana a Benjaminiwo anayamba kukantha ena mwa anthuwo, amuna a Isiraeli 30,+ pamisewu ikuluikulu yakunja kwa mzinda, ndi kuwavulaza koti sakanatha kuchira. Wina mwa misewu imeneyi unali wopita ku Beteli+ ndipo wina unali wopita ku Gibeya.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena