Oweruza 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Debora anati: “Sindilephera, tipitira limodzi. Ngakhale zili choncho, ulemerero sukhala wako kumene ukupitako, chifukwa Yehova adzapereka Sisera m’manja mwa munthu wamkazi.”+ Atatero, Debora ananyamuka n’kutsagana ndi Baraki ku Kedesi.+ Oweruza 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Sisera anakomoka, kugwa ndi kugona pakati pa mapazi ake,Iye anakomoka n’kugwa.Pamene anakomokerapo, anagwera pomwepo, atagonja.+
9 Pamenepo Debora anati: “Sindilephera, tipitira limodzi. Ngakhale zili choncho, ulemerero sukhala wako kumene ukupitako, chifukwa Yehova adzapereka Sisera m’manja mwa munthu wamkazi.”+ Atatero, Debora ananyamuka n’kutsagana ndi Baraki ku Kedesi.+
27 Sisera anakomoka, kugwa ndi kugona pakati pa mapazi ake,Iye anakomoka n’kugwa.Pamene anakomokerapo, anagwera pomwepo, atagonja.+