Yesaya 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yehova wa makamu adzam’kwapula ndi chikwapu+ ngati mmene anagonjetsera Midiyani pathanthwe la Orebi.+ Ndodo yake idzakhala panyanja+ ndipo adzaikweza m’mwamba ngati mmene anachitira ndi Iguputo.+
26 Yehova wa makamu adzam’kwapula ndi chikwapu+ ngati mmene anagonjetsera Midiyani pathanthwe la Orebi.+ Ndodo yake idzakhala panyanja+ ndipo adzaikweza m’mwamba ngati mmene anachitira ndi Iguputo.+