Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 6:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndipo Rahabi hule uja, limodzi ndi anthu a m’nyumba ya bambo ake, ndi onse amene anali naye, Yoswa sanawaphe.+ Kufikira lero, mayiyo akukhalabe pakati pa Aisiraeli,+ chifukwa anabisa anyamata amene Yoswa anawatuma kukazonda Yeriko.+

  • 1 Samueli 15:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Zili choncho, Sauli anauza Akeni+ kuti: “Nyamukani,+ muchoke pakati pa Aamaleki kuti ndisakuwonongeni pamodzi nawo. Inuyo munasonyeza kukoma mtima kosatha kwa ana onse a Isiraeli+ atatuluka mu Iguputo.”+ Choncho Akeni anachokadi pakati pa Aamaleki.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena